Yoweli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali mtundu umene walowa m’dziko langa. Mtunduwo ndi wamphamvu ndipo anthu ake ndi osawerengeka.+ Mano ndiponso nsagwadwa zawo zili ngati za mikango.+
6 Pali mtundu umene walowa m’dziko langa. Mtunduwo ndi wamphamvu ndipo anthu ake ndi osawerengeka.+ Mano ndiponso nsagwadwa zawo zili ngati za mikango.+