Ekisodo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Sizitheka! Pitani amuna amphamvu nokhanokha, mukatumikire Yehova chifukwa ndi zimene mukufuna.” Atanena mawu amenewa, anawachotsa pamaso pa Farao.+
11 Sizitheka! Pitani amuna amphamvu nokhanokha, mukatumikire Yehova chifukwa ndi zimene mukufuna.” Atanena mawu amenewa, anawachotsa pamaso pa Farao.+