Ekisodo 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima Aisiraeli.+ Nayenso Mose analemekezeka kwambiri m’dziko la Iguputo, pamaso pa atumiki a Farao ndi pamaso pa Aiguputo onse.+ Miyambo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+
3 Pamenepo Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima Aisiraeli.+ Nayenso Mose analemekezeka kwambiri m’dziko la Iguputo, pamaso pa atumiki a Farao ndi pamaso pa Aiguputo onse.+
7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+