Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo, Abulamu ananyamuka malinga ndi mmene Yehova anamuuzira, ndipo Loti ananyamuka naye limodzi. Pochoka ku Harana,+ Abulamu anali ndi zaka 75.

  • Genesis 21:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Abulahamu anali ndi zaka 100 pamene mwana wake Isaki anabadwa.

  • Genesis 25:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.

  • Genesis 47:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yakobo anayankha Farao kuti: “Zaka za moyo wanga monga mlendo m’malo osiyanasiyana zikukwana 130.+ Zaka zimenezi zakhala zowerengeka ndi zosautsa,+ ndipo sizinafike pa zaka za moyo wa makolo anga monga alendo m’malo osiyanasiyana.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena