Ekisodo 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo Aiguputo anawalondola, ndipo mahatchi onse a Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi, anayamba kuwathamangira,+ kulowa pakati pa nyanja.
23 Pamenepo Aiguputo anawalondola, ndipo mahatchi onse a Farao, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi, anayamba kuwathamangira,+ kulowa pakati pa nyanja.