Ekisodo 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo iwe, tenga ndodo yako+ ndi kutambasula dzanja lako kuloza panyanja kuti nyanjayo igawanike.+ Ukatero ana a Isiraeli adutsa pakati pa nyanja, panthaka youma.+ Machitidwe 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+
16 Ndipo iwe, tenga ndodo yako+ ndi kutambasula dzanja lako kuloza panyanja kuti nyanjayo igawanike.+ Ukatero ana a Isiraeli adutsa pakati pa nyanja, panthaka youma.+
36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+