Nehemiya 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mukamva kwina kukulira lipenga la nyanga ya nkhosa, musonkhane kumeneko, ndipo ife tidzakhala tili kumeneko. Mulungu wathu adzatimenyera nkhondo.”+ Salimo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”+“Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova wamphamvu mu nkhondo.”+
20 Mukamva kwina kukulira lipenga la nyanga ya nkhosa, musonkhane kumeneko, ndipo ife tidzakhala tili kumeneko. Mulungu wathu adzatimenyera nkhondo.”+
8 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”+“Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova wamphamvu mu nkhondo.”+