Ekisodo 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anatenga magaleta osankhidwa mwapadera 600+ ndi magaleta ena onse a Iguputo, ndipo lililonse la magaletawo munakwera asilikali.
7 Anatenga magaleta osankhidwa mwapadera 600+ ndi magaleta ena onse a Iguputo, ndipo lililonse la magaletawo munakwera asilikali.