Ekisodo 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi ana a Isiraeli anadutsa pakati pa nyanja, panthaka youma,+ madziwo ataima ngati khoma* kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+
22 Patapita nthawi ana a Isiraeli anadutsa pakati pa nyanja, panthaka youma,+ madziwo ataima ngati khoma* kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+