Numeri 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Kodi khamu la anthu oipa amenewa lidandaula motsutsana nane kufikira liti?+ Ndamva kudandaula konseko kumene ana a Isiraeli akuchita motsutsana nane.+ Yuda 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu amenewa ndi okonda kung’ung’udza,+ okonda kudandaula za moyo wawo, ongotsatira zilakolako zawo,+ ndipo amalankhula modzitukumula.+ Amatamandanso anthu ena+ n’cholinga choti apezepo phindu.
27 “Kodi khamu la anthu oipa amenewa lidandaula motsutsana nane kufikira liti?+ Ndamva kudandaula konseko kumene ana a Isiraeli akuchita motsutsana nane.+
16 Anthu amenewa ndi okonda kung’ung’udza,+ okonda kudandaula za moyo wawo, ongotsatira zilakolako zawo,+ ndipo amalankhula modzitukumula.+ Amatamandanso anthu ena+ n’cholinga choti apezepo phindu.