2 Akorinto 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Munthu wokhala ndi zambiri sanakhale ndi zopitirira muyezo, ndipo munthu wokhala ndi zochepa sanakhale ndi zocheperatu.”+
15 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Munthu wokhala ndi zambiri sanakhale ndi zopitirira muyezo, ndipo munthu wokhala ndi zochepa sanakhale ndi zocheperatu.”+