Mateyu 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Lekani kudziunjikira chuma+ padziko lapansi, pamene njenjete* ndi dzimbiri zimawononga, ndiponso pamene mbala zimathyola ndi kuba.
19 “Lekani kudziunjikira chuma+ padziko lapansi, pamene njenjete* ndi dzimbiri zimawononga, ndiponso pamene mbala zimathyola ndi kuba.