Numeri 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthuwo anali kumwazikana kukatola manawo.+ Akatero, ankawapera pamphero kapena kuwasinja mumtondo. Kenako ankawawiritsa mumphika,+ kapena kuwapanga makeke ozungulira. Kukoma kwake anali ngati keke yotsekemera* yothira mafuta.+
8 Anthuwo anali kumwazikana kukatola manawo.+ Akatero, ankawapera pamphero kapena kuwasinja mumtondo. Kenako ankawawiritsa mumphika,+ kapena kuwapanga makeke ozungulira. Kukoma kwake anali ngati keke yotsekemera* yothira mafuta.+