Ekisodo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno Mose anauza Aroni kuti: “Tenga mtsuko ndi kuthiramo mana muyezo umodzi wa omeri ndi kuuika pamaso pa Yehova kuti asungidwe m’mibadwo yanu yonse.”+
33 Ndiyeno Mose anauza Aroni kuti: “Tenga mtsuko ndi kuthiramo mana muyezo umodzi wa omeri ndi kuuika pamaso pa Yehova kuti asungidwe m’mibadwo yanu yonse.”+