Salimo 78:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani! Kodi Mulungu si uja anamenya thanthwe+Kuti madzi atuluke, kutinso patuluke mitsinje yodzaza madzi?+Koma iwo anati: “Kodi angathenso kutipatsa chakudya,+Kapena kodi angakonzere anthu ake chakudya?”+
20 Taonani! Kodi Mulungu si uja anamenya thanthwe+Kuti madzi atuluke, kutinso patuluke mitsinje yodzaza madzi?+Koma iwo anati: “Kodi angathenso kutipatsa chakudya,+Kapena kodi angakonzere anthu ake chakudya?”+