Numeri 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atanyamuka ku Alusi anakamanga msasa ku Refidimu.+ Kumeneko kunalibe madzi oti anthu amwe.