1 Samueli 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehova anayamba kuitana Samueli. Ndipo Samueli anayankha kuti: “Ine mbuyanga.”+