Aheberi 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso, zimene anaona kumeneko zinali zoopsa kwambiri moti Mose anati: “Ndikuchita mantha ndipo ndikunjenjemera.”+
21 Komanso, zimene anaona kumeneko zinali zoopsa kwambiri moti Mose anati: “Ndikuchita mantha ndipo ndikunjenjemera.”+