Oweruza 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ mundisonyeze chizindikiro kuti nditsimikize kuti ndinudi amene mukulankhula nane.+
17 Pamenepo iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima,+ mundisonyeze chizindikiro kuti nditsimikize kuti ndinudi amene mukulankhula nane.+