Salimo 69:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atsanulireni matemberero anu,+Ndipo mkwiyo woyaka moto uwagwere.+ Aheberi 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kulandira chilango chochokera kwa Mulungu wamoyo n’chinthu choopsa.+