Levitiko 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Kuchokera pa tsiku lotsatana ndi sabata, pamene munabweretsa mtolo kuti ukhale nsembe yoweyula,* muziwerenga masabata* 7,+ ndipo akwane ndendende. 1 Akorinto 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe, Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ n’kukhala chipatso choyambirira+ cha amene akugona mu imfa.+ 1 Akorinto 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma aliyense pamalo pake: Choyamba Khristu, amene ndi chipatso choyambirira,+ kenako ake a Khristu pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.
15 “‘Kuchokera pa tsiku lotsatana ndi sabata, pamene munabweretsa mtolo kuti ukhale nsembe yoweyula,* muziwerenga masabata* 7,+ ndipo akwane ndendende.
20 Komabe, Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ n’kukhala chipatso choyambirira+ cha amene akugona mu imfa.+
23 Koma aliyense pamalo pake: Choyamba Khristu, amene ndi chipatso choyambirira,+ kenako ake a Khristu pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.