Ekisodo 21:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ng’ombe ya munthu ikavulaza ndi kupha ng’ombe ya mnzake, pamenepo azigulitsa ng’ombe yamoyoyo ndi kugawana ndalamazo, ndipo azigawananso yakufayo.+
35 Ng’ombe ya munthu ikavulaza ndi kupha ng’ombe ya mnzake, pamenepo azigulitsa ng’ombe yamoyoyo ndi kugawana ndalamazo, ndipo azigawananso yakufayo.+