Levitiko 25:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 m’bale wanuyo azikhalabe ndi ufulu wowomboledwa.+ Mmodzi mwa abale ake angathe kumuwombola.+