Levitiko 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mum’tenge ngati waganyu,+ ndiponso ngati mlendo. Akutumikireni kufikira Chaka cha Ufulu.