Yesaya 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 N’chifukwa chake temberero lameza dzikolo,+ ndipo anthu okhala m’dzikolo apezeka ndi mlandu. Chotero anthu okhala m’dzikolo achepamo, ndipo anthu amene atsalamo ndi ochepa kwambiri.+
6 N’chifukwa chake temberero lameza dzikolo,+ ndipo anthu okhala m’dzikolo apezeka ndi mlandu. Chotero anthu okhala m’dzikolo achepamo, ndipo anthu amene atsalamo ndi ochepa kwambiri.+