2 Mbiri 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ataona+ kuti anthuwo adzichepetsa, mawu a Yehova anafika kwa Semaya,+ kuti: “Anthuwa adzichepetsa,+ choncho sindiwawononga. Posachedwapa ndiwapulumutsa, ndipo sinditsanulira mkwiyo wanga pa Yerusalemu kudzera m’manja mwa Sisaki.+
7 Yehova ataona+ kuti anthuwo adzichepetsa, mawu a Yehova anafika kwa Semaya,+ kuti: “Anthuwa adzichepetsa,+ choncho sindiwawononga. Posachedwapa ndiwapulumutsa, ndipo sinditsanulira mkwiyo wanga pa Yerusalemu kudzera m’manja mwa Sisaki.+