Genesis 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Numeri 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Amuna amene anatuluka mu Iguputo kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ sadzaiona nthaka imene ndinalumbirira Abulahamu, Isaki ndi Yakobo,+ chifukwa sanandimvere ndi mtima wonse.
13 Pamwamba pa makwererowo anaonapo Yehova, amene anamuuza kuti:+ “Ine ndine Yehova, Mulungu wa Abulahamu kholo lako, ndi Mulungu wa Isaki.+ Dziko limene wagonapoli ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+
11 ‘Amuna amene anatuluka mu Iguputo kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ sadzaiona nthaka imene ndinalumbirira Abulahamu, Isaki ndi Yakobo,+ chifukwa sanandimvere ndi mtima wonse.