Levitiko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tizilombo timeneti n’timene mungadzidetse nato. Aliyense wokhudza zolengedwa zimenezi zitafa azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+ Numeri 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chiwiya+ chilichonse chosavundikira bwino* chikhale chodetsedwa.
24 Tizilombo timeneti n’timene mungadzidetse nato. Aliyense wokhudza zolengedwa zimenezi zitafa azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+