Aheberi 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano popeza kuti unsembewo ukusinthidwa,+ ndiye kuti chilamulonso chifunika kusintha.+