Levitiko 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Chotero mukhale pakhomo la chihema chokumanako usana ndi usiku kwa masiku 7.+ Ndipo muyenera kuchita ulonda umene Yehova walamula,+ kuti musafe. Chifukwa n’zimene ndalamulidwa.” Ezekieli 43:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Masiku 7 amenewo akatha, kuyambira pa tsiku la 8+ kupita m’tsogolo, ansembe azidzakuperekerani nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zachiyanjano paguwali, ndipo ine ndidzasangalala nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
35 Chotero mukhale pakhomo la chihema chokumanako usana ndi usiku kwa masiku 7.+ Ndipo muyenera kuchita ulonda umene Yehova walamula,+ kuti musafe. Chifukwa n’zimene ndalamulidwa.”
27 Masiku 7 amenewo akatha, kuyambira pa tsiku la 8+ kupita m’tsogolo, ansembe azidzakuperekerani nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zachiyanjano paguwali, ndipo ine ndidzasangalala nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”