Levitiko 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tengani mbuzi yamphongo+ kuti ikhale nsembe yamachimo. Mutengenso mwana wa ng’ombe ndi nkhosa yaing’ono yamphongo,+ zonsezi zikhale za chaka chimodzi, zopanda chilema, kuti zikhale nsembe yopsereza. Levitiko 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno anaperekera nsembe anthu.+ Anatenga mbuzi yoperekera anthu nsembe yamachimo, ndipo anaipha, n’kuipereka monga nsembe yamachimo, mmene anachitira ndi nyama yoyamba ija.
3 Koma uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tengani mbuzi yamphongo+ kuti ikhale nsembe yamachimo. Mutengenso mwana wa ng’ombe ndi nkhosa yaing’ono yamphongo,+ zonsezi zikhale za chaka chimodzi, zopanda chilema, kuti zikhale nsembe yopsereza.
15 Ndiyeno anaperekera nsembe anthu.+ Anatenga mbuzi yoperekera anthu nsembe yamachimo, ndipo anaipha, n’kuipereka monga nsembe yamachimo, mmene anachitira ndi nyama yoyamba ija.