Levitiko 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tizilombo timeneti n’timene mungadzidetse nato. Aliyense wokhudza zolengedwa zimenezi zitafa azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+
24 Tizilombo timeneti n’timene mungadzidetse nato. Aliyense wokhudza zolengedwa zimenezi zitafa azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+