Ekisodo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+ Levitiko 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndiyeno wodziyeretsayo azichapa zovala zake+ ndi kumeta tsitsi lake lonse, kenako azisamba+ ndipo azikhala woyera. Akatero, angathe kulowa mumsasa, koma azikhala kunja kwa hema wake masiku 7.+ Levitiko 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso munthu wokhudza bedi lakelo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+ Numeri 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wowola phulusa la ng’ombeyo azichapa zovala zake, koma azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.+ “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa ana a Isiraeli ndi kwa mlendo wokhala pakati pawo.+
10 Ndipo Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa anthu, uwayeretse lero ndi mawa, ndipo achape zovala zawo.+
8 “Ndiyeno wodziyeretsayo azichapa zovala zake+ ndi kumeta tsitsi lake lonse, kenako azisamba+ ndipo azikhala woyera. Akatero, angathe kulowa mumsasa, koma azikhala kunja kwa hema wake masiku 7.+
5 Komanso munthu wokhudza bedi lakelo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+
10 Wowola phulusa la ng’ombeyo azichapa zovala zake, koma azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.+ “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa ana a Isiraeli ndi kwa mlendo wokhala pakati pawo.+