Deuteronomo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Samalani ndi mliri wa khate+ ndi kuonetsetsa kuti mukuchita zonse zimene ansembe achilevi adzakulangizani.+ Muzichita mosamala zonse zimene ndawalamula.+
8 “Samalani ndi mliri wa khate+ ndi kuonetsetsa kuti mukuchita zonse zimene ansembe achilevi adzakulangizani.+ Muzichita mosamala zonse zimene ndawalamula.+