Levitiko 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo.+ Azidyera m’malo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+
6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo.+ Azidyera m’malo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+