Ezekieli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu avula bambo awo.+ Iwo agona ndi mkazi wodetsedwa amene akusamba.+ Ezekieli 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iwe mwana wa munthu, pamene a nyumba ya Isiraeli anali kukhala m’dziko lawo, anali kudetsa dzikolo ndi njira zawo komanso zochita zawo.+ Pamaso panga, njira zawo zakhala ngati zonyansa za mkazi amene akusamba.+
17 “Iwe mwana wa munthu, pamene a nyumba ya Isiraeli anali kukhala m’dziko lawo, anali kudetsa dzikolo ndi njira zawo komanso zochita zawo.+ Pamaso panga, njira zawo zakhala ngati zonyansa za mkazi amene akusamba.+