Levitiko 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Aroni anapha nyama ya nsembe yopsereza, ndipo ana ake anam’patsa magazi a nyamayo. Pamenepo iye anawaza magaziwo mozungulira paguwa lansembe.+
12 Ndiyeno Aroni anapha nyama ya nsembe yopsereza, ndipo ana ake anam’patsa magazi a nyamayo. Pamenepo iye anawaza magaziwo mozungulira paguwa lansembe.+