Levitiko 23:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ili ndi sabata lopuma pa ntchito zanu zonse,+ ndipo muzidzisautsa+ madzulo pa tsiku la 9 m’mweziwo. Muzisunga sabata kuyambira madzulo kufikira madzulo tsiku lotsatira.”
32 Ili ndi sabata lopuma pa ntchito zanu zonse,+ ndipo muzidzisautsa+ madzulo pa tsiku la 9 m’mweziwo. Muzisunga sabata kuyambira madzulo kufikira madzulo tsiku lotsatira.”