Ekisodo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu ananenanso kwa Mose kuti: “Ine ndine Yehova.+ Malaki 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ine ndine Yehova, sindinasinthe.+ Inu ndinu ana a Yakobo ndipo simunatheretu.+