Levitiko 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwamuna akagonana ndi mkazi ameneyu, azikhala wodetsedwa chifukwa chakuti mkaziyo akusamba.+ Zikatero, mwamunayo azikhala wodetsedwa masiku 7, ndipo bedi lililonse limene angagonepo lizikhala lodetsedwa. Levitiko 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Usayandikire mkazi kuti um’vule+ pamene ali wodetsedwa chifukwa cha kusamba+ kwake. Ezekieli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu avula bambo awo.+ Iwo agona ndi mkazi wodetsedwa amene akusamba.+
24 Mwamuna akagonana ndi mkazi ameneyu, azikhala wodetsedwa chifukwa chakuti mkaziyo akusamba.+ Zikatero, mwamunayo azikhala wodetsedwa masiku 7, ndipo bedi lililonse limene angagonepo lizikhala lodetsedwa.