Ekisodo 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mkazi wamatsenga musam’lole kukhala ndi moyo.+ Levitiko 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Munthu wotembenukira kwa olankhula ndi mizimu+ ndi olosera zam’tsogolo,+ komwe n’kuchita mosakhulupirika kwa ine,* ndidzam’kana ndithu ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+ Mika 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Amatsenga onse m’dziko lanu ndidzawapha, ndipo pakati panu sipadzapezekanso anthu ochita zamatsenga.+
6 “‘Munthu wotembenukira kwa olankhula ndi mizimu+ ndi olosera zam’tsogolo,+ komwe n’kuchita mosakhulupirika kwa ine,* ndidzam’kana ndithu ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+
12 Amatsenga onse m’dziko lanu ndidzawapha, ndipo pakati panu sipadzapezekanso anthu ochita zamatsenga.+