Levitiko 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ng’ombe kapena nkhosa yokhala ndi chiwalo chimodzi chachitali kwambiri kapena chachifupi kwambiri kuposa chinzake,+ mungaipereke monga nsembe yaufulu, koma Mulungu sadzailandira mukaipereka pokwaniritsa lonjezo lanu.
23 Ng’ombe kapena nkhosa yokhala ndi chiwalo chimodzi chachitali kwambiri kapena chachifupi kwambiri kuposa chinzake,+ mungaipereke monga nsembe yaufulu, koma Mulungu sadzailandira mukaipereka pokwaniritsa lonjezo lanu.