Levitiko 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Mwamuna akatulutsa umuna,+ azisamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.