Numeri 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho amunawo anapita kukazonda dzikolo, kuyambira kuchipululu cha Zini+ mpaka ku Rehobu,+ kufupi ndi Hamati.+ Numeri 33:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Atanyamuka ku Ezioni-geberi anakamanga msasa m’chipululu cha Zini,+ ku Kadesi.
21 Choncho amunawo anapita kukazonda dzikolo, kuyambira kuchipululu cha Zini+ mpaka ku Rehobu,+ kufupi ndi Hamati.+