Oweruza 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anatumiza mithenga kwa mfumu ya Edomu+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu,” koma mfumu ya Edomu sinamvere. Anatumizanso mithenga kwa mfumu ya Mowabu,+ koma nayonso sinavomereze. Choncho Aisiraeli anapitiriza kukhala ku Kadesi.+
17 Kenako anatumiza mithenga kwa mfumu ya Edomu+ kuti: “Tiloleni tidutse m’dziko lanu,” koma mfumu ya Edomu sinamvere. Anatumizanso mithenga kwa mfumu ya Mowabu,+ koma nayonso sinavomereze. Choncho Aisiraeli anapitiriza kukhala ku Kadesi.+