Numeri 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Uwauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, mudzandifunse ngati sindidzachita kwa inu monga mwa zimene mwakhala mukulankhula, zimene ndadzimvera ndekha m’makutu mwangamu.+ Numeri 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mwa kuchuluka kwa masiku amene munazonda dzikolo, masiku 40,+ mudzalangidwanso kwa zaka 40+ chifukwa cha zolakwa zanu, tsiku limodzi kuwerengera chaka chimodzi, tsiku limodzi chaka chimodzi,+ kuti mudziwe kuipa kondipandukira.+
28 Uwauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, mudzandifunse ngati sindidzachita kwa inu monga mwa zimene mwakhala mukulankhula, zimene ndadzimvera ndekha m’makutu mwangamu.+
34 Mwa kuchuluka kwa masiku amene munazonda dzikolo, masiku 40,+ mudzalangidwanso kwa zaka 40+ chifukwa cha zolakwa zanu, tsiku limodzi kuwerengera chaka chimodzi, tsiku limodzi chaka chimodzi,+ kuti mudziwe kuipa kondipandukira.+