Mateyu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+ 2 Petulo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 koma anadzudzulidwa pa cholakwa chake.+ Nyama yosalankhula yonyamula katundu inalankhula ngati munthu+ ndi kulepheretsa zochita zamisala za mneneriyo.+
26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+
16 koma anadzudzulidwa pa cholakwa chake.+ Nyama yosalankhula yonyamula katundu inalankhula ngati munthu+ ndi kulepheretsa zochita zamisala za mneneriyo.+