2 Petulo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 koma anadzudzulidwa pa cholakwa chake.+ Nyama yosalankhula yonyamula katundu inalankhula ngati munthu+ ndi kulepheretsa zochita zamisala za mneneriyo.+
16 koma anadzudzulidwa pa cholakwa chake.+ Nyama yosalankhula yonyamula katundu inalankhula ngati munthu+ ndi kulepheretsa zochita zamisala za mneneriyo.+