Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuumitsa mtima wawo.+Iwo anapitiriza kuyenda mu nzeru zawo.+