Numeri 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Usikuwo Mulungu anafika kwa Balamu, n’kumuuza kuti: “Ngati anthuwa abwera kudzakuitana, nyamuka, pita nawo limodzi. Koma ukalankhule mawu okhawo amene ndikakuuze.”+
20 Usikuwo Mulungu anafika kwa Balamu, n’kumuuza kuti: “Ngati anthuwa abwera kudzakuitana, nyamuka, pita nawo limodzi. Koma ukalankhule mawu okhawo amene ndikakuuze.”+